ZAVUTA KU DPP

By Dr mwale Chipani Cha DPP chachotsa mlembi wake wankulu mayi grezelder Geffrey kamba ka mawu…

UTM IKANA JOMO OSMAN

olemba Dr Mwale Avant publications yapeza kuti Sipanathe miyezi isanu Tonse alliance chilowereni m’boma koma tikuona…

AWOTCHEDWA NDI MOTO

A Zuze Tama yemwe akuti anali m’modzi wa anthu opanga zauchifwamba aotchedwa ndi moto mpaka kufa…

MAMUNA AMWALIRA CHIFUKWA CHOGONANA MOWIRIKIZA

Mwamuna yemwe anamwalira ali mkati mwamacheza ndi mtsikana woyendayenda kuphalombe lero walowa mmanda. Imfa yomwe yabwera…

TAFINYIKA AZIMAYI NDI JANUS

olemba Dr Mwale kalekale dziko likadali mphonje tinkadalira mankhwala azitsamba kuti tichire kumatenda athu monga chinfine…

ZOMWE ZIKUCHITIKA KU MEDF

Dr Mwale MEDF ndi bungwe lomwe likupereka ngongole kwa ama business, kamba koti zonse zimayenda mundale…

PROPHET SABAO ATULUKA KUNDENDE

By Dr Mwale Mneneri odziwika bwino komanso yemwe ndi mwini wake wa Mpingo wa    Avangelic Gathering…

KUTHA KWA CHIBADE

Dr mwale Mnyamata amene anagwededza Malawi ndi maimbidwe ake abwino komanso tinyimbo take totsangala Thomas chibade…

MAGETSI ATHIMA KU QECH

Lero kummawaku ntchito zapachipatala chachikulu ku blantyre Cha Qeen Elizabeth chinali chopanda magetsi omwe anangozimà mwadzidzidzi…

KULIMBANA NDI KACHILOMBO KA CORONA KU ZOMBA

By Dr Mwale Boma lamalawi silikugona tulo polimbana ndi kachilombo ka Corona komwe kakuyambitsa matendawa a…