Lero kummawaku ntchito zapachipatala chachikulu ku blantyre Cha Qeen Elizabeth chinali chopanda magetsi omwe anangozimà mwadzidzidzi .
Anthu ambiri omwe amafuna kuchitidwa operation kapena kuti x-ray anagwira njakata poti ntchitozi zimafunika magetsi ndipo iwo sanathe kubwerera kwawo koma kugona kuti adikire mawa.
Escom yakana kuti vutoli layamba chifukwa Cha ma transformer awo koma kuti vutoli layambira kukachipinda komwe kamagawa magetsi pa chipatalachi
Kuchokera nthawi yomwe magetsi azimayi akadaulo pa zamegetsi anali akugwiragwira kuti magetsi ayake mwachangu
Nkhani yoti magetsi athima ku Chipatali inayamba kuoneka pa avant publications kummawa walero, ndipo atolankhani ambiri anali kalikiliki kufufuza kuchokera patsambali.
mukafuna Kumva nkhani zenizeni pitani pa www.avantmalawi.com
Olemba DR MWALE