KUTHA KWA CHIBADE

Dr mwale

Mnyamata amene anagwededza Malawi ndi maimbidwe ake abwino komanso tinyimbo take totsangala Thomas chibade tsopano tsogolo lake loimba latsokonekera kamba ka mowa.

Chibande amakhala mumzinda wa Lilongwe  iye amangokhalira mowa wa nkalabongo tsiku lililonse zomwe pakadali pano zampangitsa kukhala ngati chitsilu Cha mmudzi.lero chibade anaoneka ali thaphya ndi mowa pomwe anthu ena ankangomseka.

Thoma Chibade ayakiratu

Chibande ndi yemwe anaimba nyimbo monga aeiou (awa ndiwo mawu anga), wowawa ubatchala komanso anaimbapo ndi Lucius banda nyimbo yoti moyo ndi ovuta.

Zomwe akuchita chibade ndikuzionongera tsogolo chifukwa pakadali pano bwezi ali patali ndi chuma chomwe anapeza m’mbuyomu.

Zimvere wekha chibade Luso lakupulumuka.

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *