Category: Za Chichewa
BWATO LIGUBUDUZIKA KU MPOTO KWA BOMA LA NSANJE.
Ma lipoti amene akuchokera ku mpoto kwa Boma la Nsanje atsimikiza kuti Bwato lagubuduzika ndipo anthu…
BAMBO WINA WAFA ATAGWERA MUCHIMBUDZI CHOKUMBA KU BLANTYRE
Apolisi mum’zinda wa Blantyre atsimikiza za imfa yabambo wina wazaka 46 yemwe wafa atagwera muchimbudzi chokumba.…
BASI YA TAM TAM IGWIDWA PA DEDZA
Kutsatira kanema yemwe wafala pa masamba a mchezo ku m’mawaku okhudza momwe basi ya TAM TAM…