olemba Dr mwale
Munthu aliyense analengedwa kuti azabereka ndithu monga mwa chikonzero chake Cha namalenga koma malingana ndi zifukwa Zina ndi Zina kubereka matsiku ano ndikovuta kwa mabanja ena. Kodi Pali mitundi ingati ya kusabereka?
Mitundu ya kusabereka ilipo iwiri yomwe ndi primary infertility ndi secondary infertility.
Tikati primary ndekuti kukhala osabereka kuchokera pachiyambi. Pali anthu ena omwe ali pa banjakoma akhala Chaka kapena zaka mwana osabwera anthu amenewa amakhala kuti sanagwiritsepo njira ina iliyonse ya kulera komanso sanachotsepo mimba, amenewa nde Ali pa primary infertility.
Kodi chimayambitsa vutoli ndi chani?
Vutoli limayamba makamaka kwa mzimayi chifukwa chakuti zira limalephela kukhazikitsa muchiberekero momwe mwana amapangidwa chifukwa limakhala kuti likusowa poti limele kapena kuti ligwire muchiberekero, likakhala kwa matsiku angapo limangofa apa ndi pomwe mzimayi amaona period.(si azimayi onse omwe fertilization simachitika ayi,ena imakhala kuti yachitika koma zira silinagwile muchiberekero) ena zimakhala kuti mazira sakutuluka mu ma ovaries kuti apite muchiberekero, azimayi oterowa amavutika kwambiri mmimba akamayandikira kusamba.
Kukhala ndi zotupa mmimba kumatha kumpangitsa munthu kukhala osabereka, matenda asugar nawo amaonjezezera vuto lakusabereka kwa azimayi ena.kumwa komanso kusuta ndi zifukwa Zina zomwe zimafoola azimayi komanso azibambo(koma osati onse). Azimayi ena amakhala kuti muchiberekero mwawo mmatentha kwambiri zomwe zimapangitsa kuti akamagonana ndi abambo mphamvu ya abambo imatuluka yonse, ena akatenga mimba miyezi ingapo imachoka komanso ena amapititsa padera(kubereka mwana wakufa kale) zonsezi zimachitika pa primary infertility. Mauka ndi (kuyabwa malo obisika) ndi Zina zomwe zimalepheretsa azimayi kubereka.
Kwa amuna ena mavutowa amakhala kuti abwera chifukwa Cha kuchepa kwa umuna, komanso kutsekeka kwa njira yomwe mmadutsa umuna(prostrate enlargement)
Secondary infertility
Tikati secondary infertility tikuthandizani kuti munthuyo anaberekapo kamodzi kapena kawiri koma kwinako mwana sakubweranso, amakhala kuti akuyesesa koma sizikutheka chifukwa choyamba chimakhala kuti ndi mphamvu ya kulera komanso kwa amene sakutenga kulera ma hormones amakhala kuti asokonekera nde ngati mwachedwetsa kuwakonza vuto limazakhalapo mpaka kalekale. Zifukwa Zina sizikusiyana ndi zifukwa za primary infertility.
Mavuto amenewa ali ndi mankhwala ake ndipo vuto lakusabereka tsopano ndi mbiri ya kale.
kwa amene mukufuna kudziwa komanso kupeza thandizo lankhulani ndi DR MWALE pa 0991259788/0881893355