TAFINYIKA AZIMAYI NDI JANUS

olemba Dr Mwale

kalekale dziko likadali mphonje tinkadalira mankhwala azitsamba kuti tichire kumatenda athu monga chinfine ndi chifuwa

Komatu kufika muzaka za tsopanozi akadaulo adapanga mankhwala osiyanasiyana othetsera mavutowa www.avantmalawi.com ndipo anawatcha kuti janus.inde awatu ndi ma sweet omwe pakudya umangodya ngati zotsangalatsa koma ukumwa mankhwala.

Chinthu chimodzi chomwe sitimadziwa ndi chakuti pamene nzeru zako zathera za wina zimayam, atsikana nawo kudzera mukafukufuku wawo anapeza kuti Janus amabweretsa mphamvu komanso makomedwe achilendo  ku bedi omwe azibambo ambiri amagomera

Izi zinayamba kuchitika kalekale moti zimakambidwa koma anthu sankazitengera serious, koma kutsatira zomwe zachitika kuphalombe komwe mzibambo wamwalira ali mkati mwa macheza zapherezera nkhaniyi.(achipatala anapeza kuti anamwalira ndi kukoma kwambiri)

Izitu zapangitsa azimayi kudandaula kuti tsopano ndi ofinyika kumagula Janus ngati mankhwala achifuwa kapena kungodya ngati ma sweet kamba koti ogulitsa akumadziwiratu kuti  akufuna kuonjezera makomedwe,sangagule Janus komanso kudya  pagulu chifukwa alandira chitonzo  choti mukufuna kukapha ndani?

Malingana ndi kafukufuku wa za science ukuonetsa kuti munthu yemwe anamva kukoma kwenikweni kwa kugonana samakhala moyo amamwalira pompopompo.

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *