MAMUNA AMWALIRA CHIFUKWA CHOGONANA MOWIRIKIZA

Mwamuna yemwe anamwalira ali mkati mwamacheza ndi mtsikana woyendayenda kuphalombe lero walowa mmanda.

Imfa yomwe yabwera kamba kachisangalo .izi zadandaulitsa makolo a munthuyi kamba koti wafa osadwala.

Pakadali pano mtsikanayu sanamangidwe kamba koti sanachite choipa chilichonse pa imfa ya mzibamboyu.

Imfa zoterezi zimachitika koma sizochulukira choncho tisamuone nkazi amene zamchitikira izi ngati oyipa ayi komanso izi zinasokoneze buziness yake chonde azibambo muzimuona nkaziyu ngati kale yachitikayi ndi ngozi chabe.

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *