HEALTH TIPS Pali ana ambiri omwe atangobadwa mpaka pano ena ali ndi zaka ziwiri ena mpaka…
Category: Za Chichewa
MZIMAYI WINA WATAYA MWANA WAKE KU KAWALE
Apolisi ku Kawale mu Mzinda wa Lilongwe akusakasaka mzimayi yemwe sakudziwika yemwe wataya mwana wa ng’ono…
AYENDA PANSI POPITA KU NTCHITO
Olemba Dr MWALE Ma dalaivala a ma minbus mu mzinda wa Blantyre lero anyanyala ntchito zawo…
HEALTH TIP, NYAMAKAZI
Matenda a nyamakazi ndi omwe akutsautsa anthu ambiri makamaka anthu omwe zaka zawo zikuthamangira ku ma…
NCHIYANI KODI AMALAWI? BUSHIRI AKANIZIDWA KUCHITA MNSONKHANO PA BINGU STADIUM
Akulu akulu omwe akuyang’anira bwalo la Bingu aletsa mneneri sherperd Bushiri kuti asachititse msonkhano wake wa…
AKAKHALA KUNDENDE KWAZAKA 5 CHIFUKWA CHOGONANA AMUNA OKHA OKHA
Mnyamata wazaka 21 wayamba kukhala m’ndende zaka zisanu chifukwa chogona amuna okhaokha. Khothi la Dowa First…
NORMAN CHISALE ZIMUVUTA
THE MATTER IS IN COURT Mlandu wa yemwe anali wachitetezo wa president wakale a wa dziko…
OBWANDE 04 DECEMBER 2020
Mverani obwande mu audio ili mmwambayi Timakupasirani Obwande Lolemba ndi Lachisanu lililonse pa Avant publications
NKHANI ZA MPIRA
Mavuto osasimbika atha kubuka ku team ya silver strikers ngati ingayelekeze kugonja ndi team ya be…