NDI CHIFUKWA CHANI ANA ENA SAKUYENDA?

HEALTH TIPS

Pali ana ambiri omwe atangobadwa mpaka pano ena ali ndi zaka ziwiri ena mpaka 4,5 to 6 years koma sanayendebe ,kapena ena amayenda bwino bwino koma kamba kakudwala matenda ena anasiya kuyenda.

Kodi chimachitika ndi chani?

Munthu aliyense mulungu anamulenga kuti azayenda koma malingana ndi kusokonekera kwa zinthu mthupi mavutowa amachulukira.
Ana ambiri sayenda kamba koti thupi lawo limasowa mchere wa mmafupa omwe timautcha kuti calcium.

Calcium amapangitsa kuti mafupa azilimba makamaka mu ma joint momwe mumapangitsa kuti munthu apinde mafupa ndikuyamba kuyenda kapena kunyamula mwendo kapena Nkono. Izi kuti zikachitike ndi pomwenso magazi Ake amwanayo akuyenda bwino kudutsa mu mitsempha ndiku kufikira ziwalo zake zonse. Ngati izi zikuthe bwino bwino ndekuti mwanayo ayenda
komanso zimafunika kuti ma hormones ake azigwilizana bwino bwino ndi momwe nthu lake likuyendera. Mwachisankho ma hormones akalamula kuti nyamula mwendo iwe umanyamula koma ngati sanalamule nawe sunanyamule, Pena zimatheka kuti ma hormones alamula kuti ponya mwendo koma iweyo umalephera apa nde kuti system ya thupi sikutolerana

Ngati munthu ali ndi mavuto monga a kusayenda monga tatchulawa ameneyo akuyenera kuti ayambe Kumwa mankhwala omwe timati goat’s milk tablets, awa ndi mankhwala omwe Ali ndi calcium ochuluka kwambiri ndipo amapangidwa kuchokera ku mkaka wa mbuzi. Choncho ngati wina Ali ndi vuto ngati limeneri Kumwa mkaka wa mbuzi ndikothandiza kwambiri chifukwa kumathandiza kulimbitsa mafupa. Koma mukuyenera kumugukura Kaye mankhwalawa mmwanayo kapena munthuyo,komanso ngati vuto lakhalalitsa kwambiri la mwanayo , muzimpatsa goat’s milk ndi STC 30. Chifukwa goat’s milk akathandiza mmafupa pomwe STC 30 akakonza system ya ma hormones.

Alipo akulu akulu ena oti nawo sakuyenda pano kamba kanyamakazi ,apezereni calcium ndi Dyna RH basi vuto mwathana nalo.

0991259788/0881893355

DR MWALE

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *