Munthu aphedwa ku manyowe -BT

Anthu wosadziwika apha bambo wadzaka 39 ku Manyowe m’boma la Blantyre.

Izi zachitika kucha kwa lero pomwe anthu ena akuganizira kuti munthuyo mwina waphedwa ndi anthu achiwembu pomwe Ena akuti mwina munthuyo adali mulonda ndiye waphedwa pa malo womwe amagwira ntchito .

Thupi la munthuyu,lapedzeka pa mphepete mwa nsinje wa Mudi pafupi ndi bridge mdelari.

Pano a polisi atenga thupilo ndipo palibe umboni wa yemwe wachita chipongwechi.

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *