KUTHANA NDI MATENDA A HIV/AIDS POGWIRITSIRA NTCHITO STC 30

Matenda a HIV akalowa mthupi la munthu amaononga chitetezo kaye. Zikatere thupi limalowa chipwirikiti cha matenda.…

MAKOLO AKUDANDAULA NDI MKHALIDWE WA APHUNZISI APA FACE SECONDARY KU ZALEWA

olemba Dr mwale Boma la la Germany linapereka nthandizo la zamaphunziro ku boma la malawi powamangira…

OBWANDE PA 23 NOVEMBER 2020

Mverani chikalata cha Obwande lero pa 23 November 2020 Obwande amakufikirani Lolemba komanso lachisanu lililonse

AMWENYE AKUPITILIZA KUPANGIRA NKHANZA AMALAWI

olemba Dr mwale Miyezi iwili yapitayo Avant publications inalemba nkhani yokhuza company ina ku brantyre yomwe…

Obwande pa 20 November 2020

Muchikalata chawo Obwande pa 20 November 2020 alankhula za brother mmelikano (Peter Munthalika) amene abindikira ku…

KUNALINJI MSABATAYI

Olemba Dr mwale Avant publications ndi nyumba yofalitsa nkhani yomwe imadziwa kuti monga munthu sungakwanitse kumvera…

OBWANDE 13 NOVEMBER 2020

Mverani Obwand mu audio ili mmunsiyi Obwande timakupatsirani Lolemba komanso lachisanu lililonse

NGONGOLE YA NEEF(MARDEF)

by Dr mwale Boma la Malawi linapeza ndalama zochuluka zokwana 75 billion zomwe cholinga chake ndikubwereketsa…

OBWANDE 09 NOVEMBER 2020

KUNALINJI MSABATAYI?

olemba Dr Mwale Avant publications yakhala ikukupasirani nkhani zosiyanasiyana zomwe zachitika mdziko muno musabata yomwe ikuthayi.…