KUTHANA NDI MATENDA A HIV/AIDS POGWIRITSIRA NTCHITO STC 30

Matenda a HIV akalowa mthupi la munthu amaononga chitetezo kaye. Zikatere thupi limalowa chipwirikiti cha matenda. Mankhwala a ma ARVS omwe amati amaonjezera chitetezo mthupi, amaononganso chiwindi. Izi zili chomwechi poti mankhwala onse amayenera afike Kaye mu chiwindi kuti akagaike bwino asanatumizidwe komwe kuli vuto.

Ma ARVS akalowa ochuluka mthupi mwa munthu amatha kuyambitsa mavuto a body disformation kapena kuti kuphwanyika thupi. Apa tikuthandauza kuti anthu ena amatha kusintha maonekedwe awo momwe analili kale. Mwachisanzo ena amakula kuntunda kuchepa ku miyendo. Kufufuma mimba, kuphwanyika nkhope kapena matsaya , ena amaonda kwambiri ndi Zina zambiri.

Kodi nanga product yathu yotchedwa STC 30? imathandiza bwanji?

Munthu akayamba kumwa STC 30 mmaola 12 oyambirira amalowa mu system ya thupi, kuchotsa nyasi komanso ma chemicals mthupi. Kenako amayamba kuchotsa ma cells omwe anaonongeka ndi kuchulukitsa ma cells atsopano komanso athanzi. Ndiyeno amayamba kukonza chiwindi, chomwe chinaonongeka ndi mankhwala komanso ma chemicals. Chiwindi chikakonzeka basi chimayamba kutumiza ma healing properties kuthupi kuti tsopano thupi liyambe kudzikonza lokha. Pamene sabata imodzi izitha, thupi limayamba kudzibwezeretsa mwa kale mmene munthu analiri asanakhale ndi HIV. Choncho ndinganene mwa tchutchutchu kuti mankhwala a AIDS ndi amenewa basi. Koma munthu amafunika kuti amwe ma box okwana 6 kapena 8 a STC 30 Kuti athane ndi matenda amenewa

Follow us on www.avantmalawi.com

Ofunsa afunse pa 0991259788/0881893355

DR MWALE

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *