NKHANI ZA MMADERA PANO PA AVANT

*loweruka lililonse pano pa avant publication tidzimva nkhani zosiyanasiyana zochokera madera apadziko lapansi* Tiyambe ndi kwathu…

MATENDA A SUGAR

HEALTH TIP Sugar ndi matenda omwe akuvutitsa kwambiri kwa anthu akulu akulu omwe zaka zawo zadutsa…

MWATANI KODI A CDEDI?

Malingana ndi chikalata chomwe a bungwe la Center for Democrancy and Economic Development Initiative (CDEDI) yomwewasainira…

obwande 04 January 2021

Mverani Obwande mu audio ili munsiyi

MBAVA YOOPSA YOBA MA BATILE A GALIMOTO YAWONA ZOOPSA

Mbava mukuyionayi yawona zoopsa pamene imafuna kuti ikabe ma Batile a Galimoto Nkhaniyi ikuti..Bambo Kathumba omwe…

OBWANDE 01 JANUARY 2020

Mverani ndikutsatira Obwande Oyamba mu Chaka cha 2021. Happy and prosperous new year from Avant Publications

CHAKA CHOPAMBANA CHATSOPANO-2021

AVANT PUBLICATIONS BYE BYE 2020 Unali ulendo wautali kuchokera mu 2019 pomwe group ili linadziwika kwambiri…

MUNTHU ALAMULIDWA KUTI AKHALE M’NDENDE MIYEZI 18 CHIFUKWA CHOKHALA NDI CHIPHASO CHA MSCE CHABODZA

Bwalo lamilandu la First Grade Magistrate ku Phalombe lalamula bambo wina wazaka 24 kuti akakhale kundende…

NKHATABAY SOUTH CONSTITUENCY KULIBE POLICE STATION

olemba DR MWALE Kumwera kwa boma la nkhatabay komwe phungu wake ndi olemekezeka a Ken zikhale…

Munthu aphedwa ku manyowe -BT

Anthu wosadziwika apha bambo wadzaka 39 ku Manyowe m’boma la Blantyre. Izi zachitika kucha kwa lero…