HEALTH TIP
Sugar ndi matenda omwe akuvutitsa kwambiri kwa anthu akulu akulu omwe zaka zawo zadutsa 35 kupita mtsogolo. Anthu amenewa amakhala kuti adya zakudya zotsekemera kwa nthawiyo yaitali koma osatsukako mthupi mwawo kuti achotse sugar.
Choncho sugar amakha kuti akuchulukana kwambiri.
Chimachitika ndi chani sugar akachululuka ?
Choyamba dziwani kuti mthupi mwathu muli kapamba yemwe ntchito yake ndikupanga insulin yemwe amasungunula sugar kapena kuti chotsekemera chilichose chomwe chingalowe mthupi.nde sugar akalowa wambiri kapamba amalephera kupanga insulin okwanira kuti asungunule sugar.
Sugar akachuluka munthu umayamba kumva mtima kuthamanga ndipo umakhala okwiya pafupi pafupi, umamva kutentha nthupi, komanso kuotcha mapazi, ena miyendo imatupa, komanso ena amakodza pafupi pafupi.
Mavuto awa kuwalekereza amazafika poopsya kwambiri ndichifukwa chake munthu umayenera kupeza njira yoti uchotsere sugar mthupi.
Kuthana ndi matendawa
Sikophweka kuthana ndi matenda a sugar koma ukapeza mankhwala oyenera ndikutsata ndondomeko ndikopweka kuthana ndi vutoli.
Chofunikira pezani stem cell yomwe ikugwila ntchito yokonza kapamba ,akakonzeka kapamba azipanga insulin wambiri ndipo sugar olowa mthupi azisungunuridwa.
Enanu pano mumachita kuzibaya daily funso nkumati muzakhala mukutero mpaka liti? Ena simunayambe kuzibaya koma vutoli muli nalo chonde yesesani pezani stem cell Imeneyi ndipo muthandizika.
Pali anthu ena pano anasiya kudya zotsekemera kapena kumwa tea, chifukwa Cha matendawa, dziwani kuti sugar yemwe akukupwetekani ndi yemwe ali mthupi osati yemwe ali mu grocery ayi nde kusiya kumwa tea kokha osatsukako kapena kuchotsa sugar mthupi komanso kukonza kapamba sizikuthandizani ndichifukwa chakematendawo sakutha
www.avantmalawi.com
Funsani zambiri pa 0991259788/0881893355
DR MWALE