MAGETSI ATHIMA KU QECH

Lero kummawaku ntchito zapachipatala chachikulu ku blantyre Cha Qeen Elizabeth chinali chopanda magetsi omwe anangozimà mwadzidzidzi…

KULIMBANA NDI KACHILOMBO KA CORONA KU ZOMBA

By Dr Mwale Boma lamalawi silikugona tulo polimbana ndi kachilombo ka Corona komwe kakuyambitsa matendawa a…

KUNALINJI MSABATAYI?

Olemba Dr Mwale Sabata yomwe yangothayi ndi sabata yomwe mwachitika zinthu zingapo zomwe ena mwa ife…

ANYAMATA ATATU ALAMULIDWA AKHALE MU NDENDE ZAKA ZITATU

Olemba Dr Mwale Bwalo la milandu la Chikwawa First Grade Magistrate pa 13 August 2020 linalamula…

Wathetsa banja lake sabata isathe

By wongani Chipeta Mtsikana wina wamdera la la Tembwe mmudzi mwa Maganga ku Mchinji wachotsedwa kubanja…

MPINGO WA ASSEMBLIES OF GOD UGONJERA M’BUSA WA PAMALO

olemba – Dr Mwale Titha kutsimikiza kuti Mpingo wa Assemblies of God mu ulamuliro wa a…

CHILIMA ATHETSA MKANGANO WA ESCOM NDI EGENCO

olemba: Dr Mwale Lero vice President wa dziko lino a Saulosi Chilima anakumana ndi ma Kampani…

ACHINYAMATA AKWIYA NDI ZOMWE BOMA LACHITA

olemba: Dr Mwale Achinyamata ambiri mdziko muno ndi okhudzidwa ndi zomwe boma la Tonse Alliance lachita…

KUSINTHA KWA ALEMBI MU MA UNDUNA A BOMA

mulembi: Dr Mwale Chitengereni boma a mgwilizano wa Tonse president ndi wachiwiri wake akhala busy kukonza…