THE MATTER WAS IN COURT

olemba DR MWALE

Mlandu wa a Mzomera ngwira tsopano wafika kumapeto pomwe bwalo la milandu ku mzimba lagamula a busa a Christopher Mzomera Ngwira kukakhala ku ndende kwa miyezi 48 yomwe ndi zaka zinayi ndikugwira ntchito ya kalavula Gaga.

Abale ake a mzomera ngwira kunali kulira ngati aferedwa pomwe galimoto imanyamula a mzomera kupita nawo ku ndende.

Malingana ndi kafukufuku wa avant tapeza kuti a ngwira anasokoneza ndalama zokwana 250,000 zachitukuko chomangira nyumba za aphunzitsi ku mzimba Hora

Amzomera pakadali pano alinso ndi mlandu wina womwe akuyankha oyambitsa chisokonezo pa msonkhano wa MCP pomwe DPP imalamula.

www.avantmalawi.com

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *