NANKHUMWA ATENGA CHILETSO PAMENE MADZI ACHITA KATONDO KU DPP

Olemba: Dr Mwale

Akulu akulu achipani cha DPP atalengeza dzulo kuti atenga a chotsa anthu anayi mchipani chawo, anthu omwe anachotsedwawo sanakondwe ndi izi ndipo akukana kuchoka mchipanichi moti tikunena pano atenga chiletso chomwe bwalo lamilandu lapereka kuti akulu akulu a DPP abweze maganizo awo ndipo maudindo awo onse abwezeretsedwe.

Khoti lati ngati dpp inganyozere zomwe iwo anena lamulo ligwira ntchito pomangidwa kapena kulipira.www.avantmalawi.com

Izi zikuthandauza kuti pakadali pano grezelder geffrey,Nankhumwa, happie mhango komanso anthenda onse akadali muchipani Cha DPP ndipo maudindo awo abwezeretsedwa

www.avantmalawi.com

*DR MWALE*

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *