KUTHANA NDI MAUKA POGWIRITSA NTCHITO CHISOSO

KUTHANA NDI MAUKA POGWIRITSA NTCHITO CHISOSO

Azimai kodi mukuziwa kuti chisoso chimathetsanso mauka??

No matter mauka anu ndi amwano bwanji koma amatha,

Chimafunika choti muwirise masamba achisoso

madzio akawira muzaphula kuika kabigili kakang’ono ngati muma user gututu kaja

ndie mukaika madzi menemo ali amoto inu mvulani kumusiku monga azimai

chosani zonse ndipo mufundire msalu mpweya wa moto wamasamba achisoso uzilowa mkatimo

Izi mauka omwe ali mkati amatha ndithu mukatero madzi aja akazizira atengeni muzisukira pomwe pali maukapo komanso mkatimo

osaopa ndithu ndimankhwala awa alibe mvuto . .

Pangan izi kawiri pa tsiku pomatha week muzaona kusintha kwakukulu ndithu.

Ngati ndi azibambo muzingosukira madzio ali ozizira

Avant Health tips

Share this article

5 thoughts on “KUTHANA NDI MAUKA POGWIRITSA NTCHITO CHISOSO

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *