MANKHWALA AMBIRI ATHA MPHAMVU

Pamene mzipatala zambiri mankhwala akhala akusowa oti azithandizira anthu odwala zadziwika tsopano kuti mankhwala ambiri a…

Obwande 15 November 2021

Mverani obwande mu audio yotsatirayi

Obwande 12 November 2021

KHOTHI LAKANA KUPEREKA BELO KWA BAMBO DZIMADZI

Bwalo lomwe likumva mlandu wa bambo Vincent Dzimadzi womwenso amadziwika ndi dzina loti a Gabi lakana…

MADZI AKWERA MTENGO NDI 52%

Pamene mitengo ya zinthu ikupitilira kukwera monga mafuta galimoto,ophikira zakudya,magetsi ndi zina zotero  nalo bungwe logawa…

AMANGIDWA KAMBA KOSUNGA ANA KUJANDO

Anthu asanu ndi atatu amangidwa kumangochi kamba kotsekula jando nthawi ya sukulu. Mneneri wa Polisi ya…

Obwande 08 November 2021

Obwande 5 November 2021

Obwande 1 November

Obwande 29 October 2021