Obwande 9th October 2023

Atoti Manje watisiya imfa yodzidzimutsa

Zatsimikizika kuti oyimbayu amene dzina lake leni leni ndi Elias Missi Wamwalira pa Chipatala Cha Livingstonia…

*BOMA LAVOMEREZA PEMPHO LA A FELIX NJAWALA KUMANGA MWANZA STADIUM*

olemba Dr Mwale Anthu akumwanza tsopono chimwemwe chili nsaya kamba koti boma tsopano lavomereza pempho loti…

Obwande 4th October 2023

Obwande 2 October 2023

MBIRI YOCHEPA CHABE YA DR JOHN ZENUS UNGAPAKE TEMBO

John Zenus Ungapake Tembo anabadwa pa 14th September Mchaka cha 1932 M’boma la Ntcheu ku Kasinje…

Obwande 27 September 2023

10 MILLION IFUNIKA KUKONZATSO MIPANDO YOPHWANYIKA PA BINGU STADIUM

Akuluakulu oyendetsa bwalo la Bingu ati mipando 70 ndi yomwe inaonongedwa ndi ochemelera ena pa mwambo…

Obwande 25th September 2023

UTHENGA WA CHISONI KUBANJA LA A KATENGEZA

Malingana ndi a Hexin Katengeza, omwe ndi mlongo wawo wa oyimba otchuka ndi Nyimbo za Uzimu…