By Vinjeru Ngwira (Online Reporter)
Khonsolo ya mzinda wa Mzuzu yagwesa ma shop onse omwe anamangidwa kuseli kwa Mzuzu Bus depot
Avant Publication yinakwanisa kuyakhula ndi muneneli wa khonsoloyi a MacDonald Gondwa omwe asimikiza za nkhaniyi ndipo auza Avant Publication kuti onse okhuzidwa anauzidwa za chilinganizo chogwesa ma shop awo nthawi ya bwino
A MacDonald Gondwe awauzaso Avant Publication kuti khonsoloyi yipitliliza kugwesa ma shop komaso manyumba onse omwe anamangidwa malo osayenela
Werengani zambiri za nkhaniyi pa tsamba lathu potsegula http://www.avantmalawi.com🇲🇼
AVANT PUBLICATION
Share this article