NKHAN ZA MMAKWALALA MAYI WINA WACHOSOSEDWA MULOMO WAPANSI CHIFUKWA CHA NGONGORE YOKWANA 300 KWACHA M’BOMA LA THYOLO

Olemba innocent Mvundula

Nkhaniyi lkuti mmayi wina anabweleka ndalama kwa nzake yokwana 300 Malawi kwacha kwa nzake ndipo lero mwini ndalamayo anakalonjera ngongore yakeyo, koma chifukwa choti yemwe anabweleka ndalama anali alibe .

Apa mwini ndalamayo sizinamumvekere bwino ndipo anangoganiza zomuluma nzakeyo mulomo wapansi mpaka kuchosa nyama yake ndipo atatero anamusiya nzakeyo pomwepo ali mu uluru owopsya.

Ndipo anthu ena achifundo ndiwomwe anamutengera mayi ovularayo ku chipatara chaching’ono chamdelaro Koma chifukwa chovulara kwambiri anamusitha ndikupita naye chipatara chachikulu cha Thyolo.

Anthu anayesesa kuyang’ana bwinobwino pamalopo Kuti mwini ndikupezepo ka nyama komwe analuma mayi olusayo kuti mwina kanagwera pansi komano sikanapezeke ,,, lzi zachitika lero la mulungu pa 25 October 2020 mamawa.

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *