olemba Dr mwale
Mayi wa zaka 22 ku machinjiri mumzinda wa brantyre wabereka ana atatu.
Mayiyu ali pa banja ndi bambo wina koma zachisoni atangomva zoti mkazi wakewabereka ana atatu mamunayo wathawa pakhomopo kumsiya nkazi akusowa mtengo ogwira,
Avant yapeza kuti bamboyo alibe chochita ndipo Malingana ndikunena kwakeakuti amayembekezera kuti nkazi wake abereka mwana mmodzi osati atatu koma mphuno salota mayiyo wabereka ana atatu omwenso uli uchembere wake oyamba.
Anawa abadwa bwino bwino koma tsopano vuto ndi chisamaliro,Avant publications ikupempha akufuna kwabwino kuti athe kuthandiza mayiyu komanso tikupempha bambo wa anawa kuti abwerere kunyumba chifukwa onse iye di nkaziyo si olakwa koma ndi chikonzero Cha mulungu kuti abereke ana atatuwa.
www.avantmalawi.com
*DR MWALE*