ALETSA KUGULITSA CHIMANGA CHACHIWISI

Monga zimakhalira nthawi yokolora akuba amachuluka ndipo amapezelapo mwayi oyamba biziness yoguritsa chimanga angakhale kuti samakaoda koma kuba.Kutsatira madandu omwe khonsolo ya lilongwe yakhala ikulandira iwo ati kuyambira pa 4 April pasapezeke munthu ogulitsa chimanga chachiwisi kapena kuti dowe. Ndipo iwo achenjeza kuti yense opezeka azamangidwa ndikulandira chilango. Awuzeni anzanu kapena achibale omwe akupanga biziness imeneyi kuti ayime kaye angazamangidwe.Lamuloli ladza pofuna kuteteza chimanga cha anthu ochuluka omwe analima. www.avantmalawi.com *DR MWALE*

China mwa chimanga chootcha chimene chimagulitsidwa Mtauni ya Lilongwe
Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *