Anthu atatu amwalira pamenenso ena avulala modetsa nkhawa galimoto yomwe anakwera itasempha mseu wa M12 ndikugudubuzika…
Category: Za Chichewa
AWATHIRA UTSI WOKHETSA MISOZI
Apolisi ku ku City centre mu mzinda wa Lilongwe athira utsi okhetsa misozi kwa achinyamata omwe…
Mbava iwomberedwa ndi a Polisi
Apolisi awombera ndikupha chigandanga choopsa chitavulaza wapolisi wina pokana kumangidwa mdera la Makawa m’boma la Mangochi.…
Sugar wakwera Mtengo
Sitolo zina zayamba kugulitsa paketi la shuga wa Illovo wolemera kilogilamu imodzi pamtengo wa K3,500. Izi…