LOTO LA BINGU LIKUNG’AMBIKA

Loto la mtsogoleri wa kale wa dziko lino malemu Bingu Wa Mutharika loti Malawi akhale ndi…

Obwande 29 March 2021

Mverani Obwande mu audio ili m’mwambayi

CHASITSA DZAYE KUTI MZONDI AMANGIDWE

Posachedwapa takupasirani nkhani  yoti yoti mzondi mkandawire wamangidwa ku karonga. Malingana ndi malipoti akuonetsa kuti ku…

Obwande pa 26 March 2021

Obwande kuchokera pa 12 March 2021

Mverani Obwande mu audio ili m’mwambayi, tipepese chifukwa chochedwerapo kukupatsirani obwande. Izi zidachitika chifukwa Cha zovuta…

NSANJE NORTH KWAFIKA MAGETSI, KWA CHAMBULUKA

Kunali Chimwemwe Ku Nsanje North, Mdera lotchedwa Chambuluka pamene a ESCOM pansi pa utsogoleri wa Dr…

OBWANDE PA 12 MARCH 2021

mverani obwande mu audio ili munsimu

CHAKWERA ALANDIRA KATEMERA WA COVID19

Nkhani ya Katemera  wa covid19 yadzetsa manong’onong’o mdziko muno ponena kuti katemerayi ndioyipa mnthupi mwa munthu.…

A POLICE KU LILONGWE AMANGA TELALA PA MLANDU WOGWILIRA

A police amanga Raffick Issa wa zaka 29 kamba kogwilira mtsikana wa zaka 15, izi zatsimikizidwa…

OBWANDE 08 MARCH 2021