OBWANDE 18 SEPTEMBER 2020

Obwande muchikalata chawo alankhula zokhudza Mtambo Mtambo (Dpp.)

Obwande atsindika kuti Chipani cha Dpp sichimaba koma kusunga katundu.

Zinthu ngati

  1. Ndalama
  2. Mafuta
  3. Ma plot
  4. Ma Genset ndi zina zambiri
Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *