mverani obwande mu audio ili m’mwambayi pamene Deus Sandram wayamba ndikufunira Happy Nuwere kwa anthu onse otsatira Obwande.
Tisayiwala kwa zaka 18 Tsopano Obwande wapatsidwa ulemu ndi a MBC Entertainers of the year popatsidwa award ngati program yapawayilesi yosangalatsa a Malawi mu chaka chapita cha 2023.