NDIRANDE SISUNGA KAPE

OLEMBA DR MWALE

Dera lotchuka ndi malonda mu mzinda wa Brantyre labwera ndi nzeru Zina pomwe anyamata ayamba kugulitsa machesi oyeza.

Malingana ndi kuvuta kwa ndalama mu nyengo in ya covid19 amalawi akubwera ndi nzeru zosiyanasiyana kuti apeze chakudya chale lero ndipo tsopana kuĀ  ndirande kwayamba kupezeka machesi oyeza.

Kodi machesi amenewa akuwatenga kuti? Kodi  www.avantmalawi.com akumaoda ku fakitale kapena akuphwetula ma box okha?
Bwerani kundirande ndipo muzaone kuti town sisunga KAPE

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *