A Brown Mpinganjira amene amalandiridwa poyera ku MCP kudzera pa mnsonkhano oyima yima umene a President Dr Lazarus Chakwera amapanhitsa pa Lunzu, ayamikira boma la tonse alliance.
Mukulankhula kwawo iwo anene kuti Bukhu lopatulika limanenetsa kuti mmasiku otsiriza zithu zizakwera, ndipo ogulitsa malonda azizakweza katundu wawo.
Kotero kukwera kwa zithu kukupherezera kuti tili mmasiku otsiriza.
Iwo anamemeza khamu la anthu kuti akhalabe ndi chikhulupiliro ndi boma la Tonse Alliance chifukwa likuyesesa kuthana ndi mavuto a zachuma mdziko muno.
A Mpinganjira amalankhula pa Lunzu malo amene adalandiridwaso ndi Prop Arthur Peter Mutharika zaka zingapo zapitazo pamene amalowa chipani cha DPP
Zambiri tsatani pa avantmalawi.com
Share this article