Masewera a pakati pa Malawi ndi Burundi amene akuchitikira mphepete mwa Nyanja ku Livingstonia ku Salima atsala pang’ono kuyamba.
Masewerawa achibwerezawa ayamba 3 koloko ku masanaku ndipo lichititse ndi Bungwe lija la Beach Soccca Africa Cup of all Nations.
Lolemba lapitali ku Bujumbula matimuwa anakumanaso ndipo timu ya Malawi inapambana ndi zigoli 7 kwa 6
Yemwe achite mphumi kupambana lero ndiye kuti akasewera mu mpikisano wa Beach Soccer African Cup of Nations ku Egypt mwezi wa October.
Wolemba: Ekali Mputa
Zambiri tikupatsirani pa AvantSportsDesk
Share this article