Ginger ndi mankhwala omwe amathandiza kwambiri ku nkhani ya matenda a BP kapena kuti kuthamanga kwa magazi komanso mtima, koma sikuti ali 💯% ayi.
ukamamwa kapena kutafuna Ginger amamveka owotcha pa mtima zomwe zimakupangitsa munthu kusamva bwino pa mtima. ndipo ukali wake ukatsikira mmimba mwa nthawi yaitali umaotchanso matumbo ndipo zimabweretsa kutentha kwachilendo mmimba,
Ginger ali ndikuthekera koyambisa zilondaza mmimba chifukwa amapangitsa khungu lathu kukhala lopyapyala, anthu omwe amatafuna ginjer daily kapena kuti pafupipafupi amatha kukhala ndi vuto ngati akhala ndi Bala chifukwa silipola mwachangu.
Kwa azimayi ena omwe amakondanso kudya ginjer malo awo obisika kumatuluka mpweya otentha kwambiri.
Izi zimapangutsa kuti mikodzo nayo izikhala yotentha komanso yochuluka acid kwambiri. Kutentha kumenekukumapangitsa kuti akagonana ndi munthu wa Bambo malo awo obisika amakhala ngati achekeka, izi zili chimwechi chifukwa ginjer amapangitsa khungu lanu kupyapyala.
komanso kutentha kwa kumeneku kumapangisanso kuti azibambo nawo azichekeka ku chida chawo. Inu Poonam mmaona ngati ndi mauka pomwe vuto ndi ginjer wa fresh.
Mwachidure ginger amafunika kuti aziphwanyidwa Kaye ndikumuyanika kapena akapwanyidwa kuphatikiza ndi madzi otentha kenako kumwa chifukwa ukali wake wambiri umathera mmadzi.
Pewani matenda ena mthupi popewa kudya zinthu za ukali monga ginger wa fresh.
0991259788/0881893355
DR MWALE