Matenda a nyamakazi ndi omwe akutsautsa anthu ambiri makamaka anthu omwe zaka zawo zikuthamangira ku ma 40 kumapita mtsogolo. Nyamakazi imagwira mmafupa, ndipo anthu ambiri amakonda kudandaula, manja, miyendo,chiuno komanso msana.
Komatu ziwani kuti sikuti ponse pomwe mukumva ziwalo tatchulazi kupweteka nde kuti ndi nyamakazi ayi.
Kupweteka kwa mafupa kuli mmagulu mmagulu,
Emena imakhala esteopolosis, komwe ndi kuthetheka kwa mafupa mkati, ena imakhala hyperplasia komwe ndikuwawa chabe kwa mafupa, ndipo Emena imakhala nyamakazi yeniyeni sopano yomwe imabwera pakusakanikirana kwa mitundu ya zonsezi.
Chimwene chimayambitsa nyamakazi kapena kupwanya kwa mafupa ndi kugwira ntchito zolemetsa kwambiri komanso komanso kuchulukana kwa Gas mthupi.
Gasi akachululuka amakalowa mmafupa momwe amakabisala. Ndipo dziwani kuti gas ameneyu akafuna kuti atuluke amayamba kufufuma mkati mwa mafupa ndipo amapangitsa kuti mafupa anuwo azimveka kuotcha Moto. Apatu ndipomwe amang’amba mafupa kupanga timing’alu ming’alu tomwe sitingaoneke ndi maso athu, ndipo gas ameneyu amatulukira mmenemu. Apa ndi pomwe amapangitsa kuti inuyo muyambe kumba kupweteka kwa mafupa anu zomwe zimayambitsa matenda a nyamakazi.
Kuti muthane ndi vutoli mukuyenera kumatsuka mthupi mwanu pafupi pafupi ndi mankhwala otchedwa chlolophill yemwe amachotsa gas mthupi kenako muzimwa Dyna RH yemwe akathetse ululu onse komanso kutseka timing’alu tija. Anthu Ena amavutika pa Bondo kamba koti cartilage wawo anadyeka zomwe zinapangutsa Bondo kumatupa , Dyna RH amathetsa mavuto amenewa pokonzanso cartilage wanu
Munthu yemwe ali ndi vuto la mafupa lomwe lakakhala nthawi ya itali akufunika Kumwa ma boloto a Dyna RH atatu kapena 4 . Koma kwa omwe likungoyamba ndi botolo limodzi kapena awiri
Mutha kupeza mankhwalawa poimba pa 0991259788/0881893355
DR MWALE