BOMA LIYANKHA MADANDU A BON KALINDO

Boma kudzera mwa nduna ya za chuma a felix mlusu ayankha mwa amodzi mwa madandu omwe amalawi akhala akudandaula, komanso omwe anali amodzi mwa zifukwa za mademo omwe amachititsa ndi mkulu wakale wa achinyama mu chipani cha UTM a Bon Kalindo.

Kutsatira mkumano omwe a Bon kalindo anachita ndi boma anagwirizana kuti mitengo ya ma tollgate itsika kuyambira tsiku lomwelo koma izi sinathe mpaka ochita zionetserowa anakonzanso zokatseka zipata zapamnsewuzi.

Lero amalawi ayenera kukondwa kamba koti boma layankha ndikukondza ena mwa madandu awo makamaka okhudza ma tolgate

Magalimoto azilipira motere potudutsa mzipatazi tsopano

Pickup : 1000
Light vehicle : 1000
Minbus : 2000

17 _ 31 passenger/ double tyres : 4000

2 – 5 tonnes ….. : 4000

31 passengers and above 10 tonnes. : 5000

Abnormal road. : 20,000

Komanso boma launikira zinthu zina monga magalimoto omwe akukhala mozungulira dera limenero komanso omwe amadutsa pafupi pafupi ndipo mitengo yake ili motere

Light vehicles 200

Pickup 200

Minbus. 400

Ena onse. 800

10 tonne above. 1000

Bomala laganiziranso kwa magalimoto onyamula maliro kuti azilipira kuti azilipira mitengo yotsikayi.

Mitengo iyi ikuyenera kuyamba pa 12 January 2022

www.avantmalawi.com

DR MWALE

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *