olemba Vinjeru Ngwira
Osewera kutsogolo kwa team ya Polokwane City komaso timu ya dziko lino (flames) Kuda fada ikena Myaba wabwera poyela ndikupepasa kutimu yake ya Polokwane City, izi zikuza pomwe ubale wa Kuda Myaba ndi akulu-akulu a team ya Polokwane City sunali kuyenda bwino,,
Kuda Myaba wapepesa ku team ya Polokwane komaso kulonjeza kutumikila team ya Polokwane ndi mtima wonse..
Kuda Myaba yabweraso payela ndikupepasa kwa mphunzitsi wa team yadziko lino (flames) Meke Mwase komaso Osewera wakale wa team ya Be forward Wonderer komaso Malawi Esau Kanyenda pa kusagwirizana komwe kunali pakati pawo .
Share this article