UTHENGA WA MALIRO

Malawi akupitilira kukhala anthu okhumudwa tsiku ndi tsiku pomwe akutaya achibale mosayembekezereka.

Lero amalawi ataya MR Albert Banda omwe amagwira ntchito ku nyumba yolemba ndikutsindikiza nkhani ya Nation Publications Limited, ngati Marketing Manager.

MR Albert anali mwana wa achimwe awo a Aleke Banda( GREAT BANDA) ndipo kwawo ndi ku Tukombo m’boma la Nkhata -bay.

Mzimu wawo uwuse mu mtendere.

www.avantmalawi.com

*DR MWALE*

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *