Muchikalata chawo Obwande pa 20 November 2020 alankhula za brother mmelikano (Peter Munthalika) amene abindikira ku Mangochi komanso mfiti yayikazi (Grezeder Jeffrey) amene adalankhula motumbwaa kuti iwo ndi mfiti yayikazi.
Obwande polemba chikalata chawo adandaula ndi zimene lidachita dziko la South Africa poyimitsa ndege ya President Chakwera pokayikira kuti imathawitsa a Bushiri.
Obwande wati mkofunika dziko la south Africa kuti lipepese ku mtundu wa a malawi pachipongwe chomwe adachita kuchotsa ulemu wa Mtsogoleri wa dziko (pakumusecha) ndi nduna zake
Share this article