A Alex Major yemwe ndi wachinyamata wa chipani cha MCP walembera kalata mlembi wamkulu wachipanichi a Eisenhower Mkaka kuti awabwenzeretse m’chipani mwansanga ndipo kupanda kutero akamang’ala ku bwalo la milandu.
Koma avant publications yapeza kuti a Mkaka sakuziwa chilichonse pa nkhaniyo kamba koti sanalandire chikalatati.
A mkaka sabata latha anachotsa a major mchipanichi kamba koti amachita zosokoneza komanso kulankhula zosakhala bwino za president wa dziko lino ndi ulamuliro wake.
www.avantmalawi.com
DR MWALE
Share this article