KODI STEM CELL NDI CHANI

olemba Dr mwale

anthu ambiri akhala akumakamba za ma stem cell komanso kugulitsa mankhwala oterewa koma anthu sakumvetsa kuti ma stem cell ndi chani kweni kweni?

Stem cell ndi  kachinthu komwe kamapangiwa mwachilengedwe kuti kazipanga zinthu(ziwalo) zizanze mthupi mwathu,(zitha kusamveka bwino muchichewa) koma cell imeneyi ndi cell yomwe imapanga ma cell onse mthupi la munthu mwachinsanzo kuti munthu apangidwe kamayamba ndi ka embryo. Nde embryo ndi imene imapanga cell yoti mutu upangidwe,mtima,khungu, mapapo ,manja ziwalo zobisika ndi Zina zotere.

Pali mitundi itatu ya ma stem cell yomwe ilipo ndi embryonic stem cell, adult stem cell ndi induced stem cell.

Munthu ukadwala ndekuti ma cell achiwalo chimenecho sakugwira bwino ntchito.

Mwachisanzo mukadwala mtima ziwani kuti ma cell a mtima sakugwira ntchito, chimodzimodzi udwala,miyendo, sugar bp, cancer, kusabereka, maso,makutu ndi Zina zotere ziwani kuti ma cell a ziwalo zimenezo adasiya kugwira ntchito.

*Kodi ma cell akasiya kugwira ntchito tikuyenera kutani?*

Ukangokhala chete nawe umakhala kuti zako zatha koma pamafunika kuti upeze mankhwala oti akuthandize iweyokuti ma cell amenewo abwerere mchimake koma ngati sakubwerera nawenso sungachire. Kuchipatala amatipatsa mankhwala oletsa ululu mmalo mwa kubwezeretsa ma cell.

Akatswiri a za science tsopano anapanga makhwala omwe ali ndi ma stem cell omwe anakonza ma cell onse akufa mthupi mwanu. Mukangobwezeretsa ma cells mavuto onse amakhala kuti atha. Zili ndi inu kupitiliza ndi ma pain killer kapena kupeza ma stem cell.
0991259788/0881893355

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *