A NORMAN CHISALE AMANGIDWASO KACHINAYI

Olemba DR MWALE

Norman Chisale wamangidwanso pa mlandu wakuti anagwiritsa ntchito certificate ya chinyengo polowa ntchito ya usilika kalelo.

www.avantmalawi.com yapeza kuti lero achisale akuyembekezeka kukaonekera ku bwalo la milandu kuti akamve ngati nkoyenera kuwapatsa bail kapena ayi.koma asanatero police inapita kundende ya maula kukawauza achisale za kumangidwabe kwawo kwachinayi ndipo awalemba sitetementi Achisale ngati zingatheke kuti apatsidwe Belo saloledwa kupitabe kunyumba koma kukakhalabe ku maula.

Share this article

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *