olemba Dr mwale
Phungu wakale wa nyumba ya malamulo wa dera la Kumpoto kwa boma la Neno a Henry Zembere amwalira atadwala kwa nthawi yayitali matenda a Sugar komanso kuthamanga kwambiri kwa magazi (high blood pressure BP)
.
a Zembere anakhalapo Phungu wa chipani Cha UDF ku nyumba ya malamulo mu www.avantmalawi.com ulamuliro wa Dr Bakili Muluzi kuchokera mchaka cha 1994 mpaka 1999.
Malemuwo amwalira ndi zaka 81 ndipo asiya ana 7.
Mwambo wa maliro uchitika mawa m’mudzi mwa Kaponda m’bomalo.
Share this article