olemba Dr mwale
mwayi kwa onse ochita malonda ogulitsa ice cream, ma apples komanso zipatso zosiyanasiyana. Ife a *Nyanja investment* tsopano tikupezeka ndi katundu uyu motere.
ma apple amitundu yonse red and green . Ma apples amenewa amakhala, 135, ena 150, ena 165 ndipo ena amakhalamo 180 mu box. Ife tikuodetsa pa mtengo wa *K18,000* per box.
*Big orangaes* ife timapezekanso ndi ma oranges 🍊 omwe amachokera ku South Africa. Pa mtengo wa *k6000 per pack.
*Ice cream pawders* tili ndi mitundu mitundu ya ice cream pawders yonse yomwe inu mungafune yakuntima kwanu monga chocolate, strawberry komanso vanilla. Packet imodzi timagulitsa/kuodetsa @ K5,500 ndipo mu box mmakhala ma packet 16 . Box yonse ndi *K75,000.
Tilinso ndi ma ice cream cones omwe imodzi timagulitsa @k45 koma box yonse timagulitsa/kuodetsa @ *K40,000
Timapezeka ku Lilongwe ku area 23
Nkhani yabwino ndiyakuti tili ndi free delivery katundu wathuyi konse komwe muli mmalawi muno.
Mukafuna katunduyi musazengereze Imbani foni pa
0991259788 kapena 0881893355